Community Self Management, Empowerment and Development
English version of this poem
..
.
..........
.
Pitani ku anthu
Poem by Lau Tsu
translated by Patricia Bulanda Mbewe
Tao Te Ching, Chapter 17
edited by Phil Bartle
 Pitani
Ku anthu;
Khalani pakati pao;
Akondeni;
Phunzilani kwa iwo;
Yambilani pomwe ali;
Gwirani nao nchinto;
Manga dzomwe alinazo.
. . .
Koma pa atsongoleli awo,
Nchinto ikatha,
Nchito yatha,
Anthu onse adzathi:
"Thazichitila theka"
                             Lao Tsu
.
––»«––